1 Atesalonika 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu akufuna kuti mukhale oyera+ mwa kupewa dama.*+ Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+