Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu+ wanu ubwere. Chifuniro chanu+ chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano.+ Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+ 1 Petulo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+ 1 Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso, dziko likupita limodzi ndi chilakolako chake,+ koma wochita chifuniro+ cha Mulungu adzakhala kosatha.+
39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+
2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+
17 Ndiponso, dziko likupita limodzi ndi chilakolako chake,+ koma wochita chifuniro+ cha Mulungu adzakhala kosatha.+