Mateyu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.” Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”
22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.”
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo m’chimake.+ Kodi sindiyenera kumwa za m’kapu imene Atate wandipatsa,+ zivute zitani?”