Mateyu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Sikuti aliyense wonena kwa ine kuti, ‘Ambuye, Ambuye,’ adzalowa ufumu wakumwamba ayi, koma yekhayo amene akuchita+ chifuniro cha Atate wanga wakumwamba.+ 1 Petulo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+
21 “Sikuti aliyense wonena kwa ine kuti, ‘Ambuye, Ambuye,’ adzalowa ufumu wakumwamba ayi, koma yekhayo amene akuchita+ chifuniro cha Atate wanga wakumwamba.+
2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+