Miyambo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lilime lodekha lili ngati mtengo wa moyo,+ koma lilime lachinyengo limapweteketsa mtima.+ Mlaliki 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mawu otsitsa a anthu anzeru amamveka kwambiri+ kuposa kukuwa kwa munthu amene akulamulira pakati pa anthu opusa.+ Yakobo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.
17 Mawu otsitsa a anthu anzeru amamveka kwambiri+ kuposa kukuwa kwa munthu amene akulamulira pakati pa anthu opusa.+
13 Kodi pakati panu pali aliyense wanzeru ndi womvetsa zinthu? Ameneyo ayenera kukhala ndi khalidwe labwino limene limasonyeza kuti amachita chilichonse+ mofatsa ndipo kufatsa kwake kumachokera mu nzeru.