Maliko 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero iye anawafunsa kuti: “Kodi nanunso ndinu osazindikira ngati iwo aja?+ Kodi inunso simudziwa kuti palibe chochokera kunja kwa thupi n’kudutsa m’thupi mwa munthu chimene chingamuipitse, Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+
18 Chotero iye anawafunsa kuti: “Kodi nanunso ndinu osazindikira ngati iwo aja?+ Kodi inunso simudziwa kuti palibe chochokera kunja kwa thupi n’kudutsa m’thupi mwa munthu chimene chingamuipitse,
18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+