Salimo 143:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+ Miyambo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 udzamvetsa tanthauzo la kuopa+ Yehova ndipo udzamudziwadi Mulungu.+ Yohane 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati munthu akufuna kuchita chifuniro cha amene ananditumayo, adzadziwa za chiphunzitsochi ngati chili chochokera kwa Mulungu,+ kapena ngati ndimalankhula za m’maganizo mwanga.
10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+
17 Ngati munthu akufuna kuchita chifuniro cha amene ananditumayo, adzadziwa za chiphunzitsochi ngati chili chochokera kwa Mulungu,+ kapena ngati ndimalankhula za m’maganizo mwanga.