Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Mlaliki 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+