Miyambo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usadzitame ndi zamawa+ chifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.+ Mlaliki 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+ Mlaliki 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti palibe akudziwa zimene zidzachitike,+ popeza ndani angamuuze mmene zidzachitikire? Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+