Yobu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana ake amalemekezedwa, koma iye sadziwa zimenezo.+Iwo amakhala opanda pake, koma iye sawaganizira. Miyambo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usadzitame ndi zamawa+ chifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.+ Mlaliki 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti palibe akudziwa zimene zidzachitike,+ popeza ndani angamuuze mmene zidzachitikire? Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
21 Ana ake amalemekezedwa, koma iye sadziwa zimenezo.+Iwo amakhala opanda pake, koma iye sawaganizira.
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+