Yakobo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+
14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+