Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mkaziyu atatsala pang’ono kumwalira, amayi amene anaima pambali pake anayamba kulankhula kuti: “Usachite mantha, pakuti wabereka mwana wamwamuna.”+ Koma iye sanayankhe kapena kuikirapo mtima.

  • Salimo 39:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Zoonadi, munthu amayenda ngati chithunzithunzi.+

      Ndithudi, anthu amapokosera pachabe.+

      Munthu amaunjika zinthu ndipo sadziwa amene adzazitute.+

  • Mlaliki 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndiponso nsanje yawo zatha kale,+ ndipo alibenso gawo mpaka kalekale pa chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano.+

  • Yesaya 63:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena