Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Mlaliki 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndinafuna kumvetsetsa ndi kuganizira mozama zinthu zonsezi:+ Anthu olungama ndiponso anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali m’dzanja la Mulungu woona.+ Anthu sadziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.+
9 Ine ndinafuna kumvetsetsa ndi kuganizira mozama zinthu zonsezi:+ Anthu olungama ndiponso anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali m’dzanja la Mulungu woona.+ Anthu sadziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.+