Deuteronomo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+ 1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,+Umudalire+ ndipo iye adzachitapo kanthu.+
3 Iye analinso kukonda anthu ake.+Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+