Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Salimo 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Sonkhanitsani okhulupirika anga kwa ine,+Amene achita pangano mwa kupereka nsembe.”+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”