Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye analinso kukonda anthu ake.+

      Oyera awo onse ali m’manja mwanu.+

      Iwowa anakhala pansi, pamapazi panu.+

      Anayamba kulandira ena mwa mawu anu.+

  • 2 Mbiri 29:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano mfumu Hezekiya+ inadzuka m’mawa kwambiri+ n’kusonkhanitsa akalonga+ a mzindawo, n’kupita kunyumba ya Yehova.

  • Salimo 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+

      Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+

      Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+

  • Miyambo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+

  • Yesaya 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ine ndapereka lamulo kwa opatulika anga.+ Ndaitananso anthu anga amphamvu oti asonyeze mkwiyo wanga.+ Amenewa ndi anthu anga okondwa kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena