Nehemiya 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zochuluka+ ndipo anasangalala+ pakuti Mulungu woona anawachititsa kusangalala kwambiri.+ Akazi+ ndi ana+ nawonso anasangalala, mwakuti phokoso la chisangalalo cha Yerusalemu linamveka kutali.+ Salimo 126:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 126 Pamene Yehova anasonkhanitsa ndi kubwezeretsa ogwidwa ukapolo a Ziyoni,+Tinakhala ngati tikulota.+
43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zochuluka+ ndipo anasangalala+ pakuti Mulungu woona anawachititsa kusangalala kwambiri.+ Akazi+ ndi ana+ nawonso anasangalala, mwakuti phokoso la chisangalalo cha Yerusalemu linamveka kutali.+
126 Pamene Yehova anasonkhanitsa ndi kubwezeretsa ogwidwa ukapolo a Ziyoni,+Tinakhala ngati tikulota.+