Salimo 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha inu,+Ndidzaimba nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+ Salimo 92:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+
2 Ndidzakondwera ndi kusangalala chifukwa cha inu,+Ndidzaimba nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina lanu, inu Wam’mwambamwamba.+
4 Pakuti mwandichititsa kusangalala, inu Yehova, chifukwa cha zochita zanu.Ndimafuula mosangalala chifukwa cha ntchito ya manja anu.+