Nehemiya 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zambiri ndipo anasangalala+ chifukwa Mulungu woona anawachititsa kuti asangalale kwambiri. Akazi ndi ana nawonso anasangalala+ moti phokoso lachisangalalo ku Yerusalemu linamveka kutali.+
43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zambiri ndipo anasangalala+ chifukwa Mulungu woona anawachititsa kuti asangalale kwambiri. Akazi ndi ana nawonso anasangalala+ moti phokoso lachisangalalo ku Yerusalemu linamveka kutali.+