Yeremiya 51:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Konzekeretsani mitundu ya anthu kuti imuthire nkhondo, mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake, atsogoleri ake onse ndi madera onse olamulidwa ndi aliyense wa amenewa.
28 Konzekeretsani mitundu ya anthu kuti imuthire nkhondo, mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake, atsogoleri ake onse ndi madera onse olamulidwa ndi aliyense wa amenewa.