Yesaya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide. Yeremiya 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 mafumu onse a Zimiri, mafumu onse a Elamu,+ mafumu onse a Amedi,+ Danieli 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ndipo Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ali ndi zaka pafupifupi 62.
17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide.