2 Pali masomphenya ochititsa mantha+ amene ndaona: Mtundu wochita chinyengo ukuchita zachinyengo, ndipo mtundu wolanda zinthu ukulanda zinthu.+ Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndathetsa kuusa moyo konse kumene mzindawo unachititsa.+