Yeremiya 50:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha+ kuchitira Babulo+ ndiponso zimene waganiza kuti achitire dziko la Akasidi.+ Ndithudi chilombo chidzakokera ana a nkhosa uku ndi uku,+ ndipo chidzawononga malo awo okhala chifukwa cha anthuwo.+
45 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha+ kuchitira Babulo+ ndiponso zimene waganiza kuti achitire dziko la Akasidi.+ Ndithudi chilombo chidzakokera ana a nkhosa uku ndi uku,+ ndipo chidzawononga malo awo okhala chifukwa cha anthuwo.+