Yesaya 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo. Yeremiya 51:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+
20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo.
43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+