Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Ine ndidzawaukira,”+ watero Yehova wa makamu.

      “M’Babulo ndidzachotsamo dzina,+ anthu otsala, ana, ndi mbadwa,”+ watero Yehova.

  • Yeremiya 50:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti mtundu wina wabwera kudzamuukira kuchokera kumpoto.+ Umenewu ndi mtundu umene wasandutsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa, moti m’dzikoli mulibe aliyense wokhalamo.+ Anthu ndiponso ziweto zathawa.+ Zonse zapita.”+

  • Yeremiya 50:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, m’dzikomo simudzakhalanso anthu+ ndipo dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayang’ana modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+

  • Yeremiya 51:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Dziko ligwedezeke ndi kumva ululu waukulu,+ chifukwa Yehova waganiza zokhaulitsa Babulo kuti dzikolo likhale chinthu chodabwitsa, lopanda munthu wokhalamo.+

  • Chivumbulutso 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena