Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+ Salimo 109:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mbadwa zake ziphedwe ndi kuchotsedwa m’dziko.+Dzina lawo lifafanizidwe mu m’badwo wotsatira.+ Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+