Yeremiya 51:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dziko ligwedezeke ndi kumva ululu waukulu,+ chifukwa Yehova waganiza zokhaulitsa Babulo kuti dzikolo likhale chinthu chodabwitsa, lopanda munthu wokhalamo.+
29 Dziko ligwedezeke ndi kumva ululu waukulu,+ chifukwa Yehova waganiza zokhaulitsa Babulo kuti dzikolo likhale chinthu chodabwitsa, lopanda munthu wokhalamo.+