Zefaniya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.
3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.