Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide.

  • Yeremiya 51:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+

  • Yeremiya 51:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 “Kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zidzafuula mosangalala chifukwa cha kugwa kwa Babulo,+ pakuti ofunkha zinthu zake adzafika kuchokera kumpoto,”+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena