Yeremiya 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti mtundu wina wabwera kudzamuukira kuchokera kumpoto.+ Umenewu ndi mtundu umene wasandutsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa, moti m’dzikoli mulibe aliyense wokhalamo.+ Anthu ndiponso ziweto zathawa.+ Zonse zapita.”+ Yeremiya 50:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto. Mtundu wamphamvu+ ndi mafumu akuluakulu+ adzautsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
3 Pakuti mtundu wina wabwera kudzamuukira kuchokera kumpoto.+ Umenewu ndi mtundu umene wasandutsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa, moti m’dzikoli mulibe aliyense wokhalamo.+ Anthu ndiponso ziweto zathawa.+ Zonse zapita.”+
41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto. Mtundu wamphamvu+ ndi mafumu akuluakulu+ adzautsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+