Yeremiya 50:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto.Mtundu wamphamvu ndi mafumu akuluakulu+ adzakonzekera kuukiraKuchokera kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi.+
41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto.Mtundu wamphamvu ndi mafumu akuluakulu+ adzakonzekera kuukiraKuchokera kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi.+