Yesaya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo akuchokera kudziko lakutali.+ Akuchokera kumalekezero a kumwamba. Yehova akubwera ndi zida za mkwiyo wake, kuti asakaze dziko lonse lapansi.+
5 Iwo akuchokera kudziko lakutali.+ Akuchokera kumalekezero a kumwamba. Yehova akubwera ndi zida za mkwiyo wake, kuti asakaze dziko lonse lapansi.+