Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+ Yeremiya 51:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Iwe ndiwe chibonga changa, zida zanga zankhondo.+ Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya mitundu ya anthu kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzawononga maufumu.
11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+
20 “Iwe ndiwe chibonga changa, zida zanga zankhondo.+ Kudzera mwa iwe ndidzaphwanya mitundu ya anthu kukhala zidutswazidutswa. Kudzera mwa iwe ndidzawononga maufumu.