Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire.+ Iwowa amaona kuti siliva si kanthu, ndipo sasangalala ndi golide.

  • Yeremiya 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ agwiritsa ntchito anthu anga monga antchito awo.+ Chotero ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo ndiponso mogwirizana ndi ntchito za manja awo.’”+

  • Yeremiya 51:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Kwezani mtengo wa chizindikiro amuna inu.+ Imbani lipenga pakati pa mitundu ya anthu. Konzekeretsani+ mitundu ya anthu yoti imuthire nkhondo. Muitanireni maufumu a ku Ararati,+ ku Mini ndi ku Asikenazi.+ Muikireni wolemba anthu usilikali. Mubweretsereni mahatchi+ ngati dzombe lokhala ndi ubweya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena