Genesis 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’mwezi wa 7,* pa tsiku la 17 la mweziwo, chingalawacho+ chinaima pamapiri a Ararati.+ Yeremiya 50:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto. Mtundu wamphamvu+ ndi mafumu akuluakulu+ adzautsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto. Mtundu wamphamvu+ ndi mafumu akuluakulu+ adzautsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+