Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu a mitundu ina adzawatenga n’kubwerera nawo kwawo ndipo nyumba ya Isiraeli idzatenga anthuwo kuti akhale awo m’dziko la Yehova, ndiponso kuti akhale antchito awo aamuna ndi aakazi.+ Iwo adzagwira+ anthu amene anawagwira n’kupita nawo kudziko lina ndipo azidzalamulira anthu amene anali kuwagwiritsa ntchito.+

  • Yeremiya 50:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 “Taona! Mtundu wa anthu ukubwera kuchokera kumpoto. Mtundu wamphamvu+ ndi mafumu akuluakulu+ adzautsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Yeremiya 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Babulo wakhala kapu yagolide m’dzanja la Yehova+ ndipo waledzeretsa dziko lonse lapansi.+ Mitundu ya anthu yaledzera ndi vinyo wake.+ N’chifukwa chake mitundu ya anthu ikuchita zinthu zamisala.+

  • Habakuku 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chifukwa chakuti iwe unafunkha mitundu yambiri ya anthu, anthu onse otsala a m’mitunduyo adzafunkha zinthu zako.+ Iwo adzateronso chifukwa unakhetsa magazi a mtundu wa anthu komanso unachitira chiwawa dziko lapansi, tauni ndi anthu onse okhala mmenemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena