Chivumbulutso 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+ Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+
3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+