Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Moredekai Myuda anali wachiwiri+ kwa Mfumu Ahasiwero ndipo anali wotchuka pakati pa Ayuda. Khamu lonse la abale ake linali kukondwera naye. Iye anali kuchitira zabwino anthu a mtundu wake ndi kulankhula zamtendere+ kwa ana awo onse.

  • Danieli 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+

  • Danieli 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’kupita kwa nthawi, Danieli anaonetsa kuti anali wodziwa kugwira ntchito bwino+ kuposa nduna zonse zapamwamba ndi masatarapi onse, chifukwa anali ndi luso lodabwitsa+ ndipo mfumu inali kuganiza zomukweza kuti akhale pamwamba pa wina aliyense mu ufumuwo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena