16 Ndamvanso kuti iweyo umatha kumasulira zinthu+ ndi kumasula mfundo. Tsopano ngati ungathe kuwerenga mawuwa ndi kundiuza kumasulira kwake, ndikuveka zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi, ndipo ndikuika kukhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.”+