Ezara 2:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 kupatulapo akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi 200. Yesaya 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira.+ Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+ ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yokongola.+ Yesaya 61:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Alendo adzabwera n’kumaweta ziweto zanu.+ Anthu ochokera kwina+ adzakhala olima minda yanu ndi osamalira minda yanu ya mpesa.+ Zekariya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndikuwaloza mowaopseza,+ ndipo adzatengedwa ndi akapolo awo kuti akhale chuma cha akapolowo.’+ Ndithu, anthu inu mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma.+
65 kupatulapo akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi 200.
7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira.+ Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+ ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yokongola.+
5 “Alendo adzabwera n’kumaweta ziweto zanu.+ Anthu ochokera kwina+ adzakhala olima minda yanu ndi osamalira minda yanu ya mpesa.+
9 Ine ndikuwaloza mowaopseza,+ ndipo adzatengedwa ndi akapolo awo kuti akhale chuma cha akapolowo.’+ Ndithu, anthu inu mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma.+