Esitere 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku limenelo, Mfumu Ahasiwero inapereka kwa mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ amene anali kuchitira nkhanza Ayuda.+ Ndipo Moredekai anabwera pamaso pa mfumu chifukwa Esitere anali atauza mfumu ubale umene unalipo pakati pawo.+ Esitere 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai. Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.
8 Tsiku limenelo, Mfumu Ahasiwero inapereka kwa mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ amene anali kuchitira nkhanza Ayuda.+ Ndipo Moredekai anabwera pamaso pa mfumu chifukwa Esitere anali atauza mfumu ubale umene unalipo pakati pawo.+
3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai.
14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.