8 Chifukwa chakuti iwe unalanda zinthu za mitundu yambiri ya anthu,
Anthu onse otsala a mitundu imeneyo adzalanda zinthu zako.+
Adzachita zimenezi chifukwa unakhetsa magazi a anthu,
Ndiponso unachitira chiwawa dziko lapansi,
Komanso mizinda ndi anthu onse okhala mmenemo.+