Yeremiya 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzakuutsira owononga+ ndipo aliyense wa iwo adzabwera ndi zida zake.+ Iwo adzadula mitengo yako yabwino kwambiri ya mkungudza+ ndi kuigwetsera pamoto.+
7 Ndidzakuutsira owononga+ ndipo aliyense wa iwo adzabwera ndi zida zake.+ Iwo adzadula mitengo yako yabwino kwambiri ya mkungudza+ ndi kuigwetsera pamoto.+