Yesaya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndapereka lamulo kwa opatulika anga.+ Ndaitananso anthu anga amphamvu oti asonyeze mkwiyo wanga.+ Amenewa ndi anthu anga okondwa kwambiri.
3 Ine ndapereka lamulo kwa opatulika anga.+ Ndaitananso anthu anga amphamvu oti asonyeze mkwiyo wanga.+ Amenewa ndi anthu anga okondwa kwambiri.