Yesaya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndauzidwa masomphenya ochititsa mantha akuti: Mtundu wachinyengo ukuchita zachinyengo,Ndipo mtundu wowononga ukuwononga. Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndidzathetsa mavuto onse amene mzindawo unachititsa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:2 Yesaya 1, ptsa. 216-217 Ulosi wa Danieli, tsa. 110
2 Ndauzidwa masomphenya ochititsa mantha akuti: Mtundu wachinyengo ukuchita zachinyengo,Ndipo mtundu wowononga ukuwononga. Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndidzathetsa mavuto onse amene mzindawo unachititsa.+