Salimo 53:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+ Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Salimo 126:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sonkhanitsani ndi kubwezeretsa gulu lathu logwidwa ukapolo inu Yehova,+Ngati mmene mumabwezeretsera madzi m’mitsinje ya ku Negebu.+
6 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+
85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+
4 Sonkhanitsani ndi kubwezeretsa gulu lathu logwidwa ukapolo inu Yehova,+Ngati mmene mumabwezeretsera madzi m’mitsinje ya ku Negebu.+