Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, dziko lanu mwalisonyeza kukoma mtima.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ukapolo.+
85 Inu Yehova, dziko lanu mwalisonyeza kukoma mtima.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ukapolo.+