Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.” Luka 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga,+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha inu.+ Yohane 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndipo osati kufera mtundu chabe, komanso kuti asonkhanitse pamodzi+ ana a Mulungu obalalika.+
8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.”
20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga,+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha inu.+