Maliko 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anatenga kapu ndi kuyamika, n’kuipereka kwa iwo, ndipo onse anamwa.+ 1 Akorinto 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?
16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?