Mateyu 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anatenga kapu+ ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo n’kunena kuti: “Imwani nonsenu.+ Luka 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno analandira kapu+ ndi kuyamika, kenako anati: “Landirani kapu iyi, nonse imwani mopatsirana.
17 Ndiyeno analandira kapu+ ndi kuyamika, kenako anati: “Landirani kapu iyi, nonse imwani mopatsirana.